1 Samueli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+ Salimo 127:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Taonani! Ana ndi cholowa chochokera kwa Yehova.+Chipatso cha mimba ndicho mphoto.+ Hoseya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ulemerero wa Efuraimu udzauluka ngati mmene imaulukira mbalame,+ moti sipadzakhalanso kubereka, kukhala ndi pakati, kapena kutenga pakati.+
5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+
11 Ulemerero wa Efuraimu udzauluka ngati mmene imaulukira mbalame,+ moti sipadzakhalanso kubereka, kukhala ndi pakati, kapena kutenga pakati.+