Mateyu 27:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero anamulavulira+ ndi kutenga bango lija ndi kuyamba kum’menya nalo m’mutu.