Yeremiya 48:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “‘Mowabu adzawonongedwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu+ chifukwa wadzikweza pamaso pa Yehova.+ Ezekieli 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu inu munalankhula modzitama kwa ine ndi pakamwa panu.+ Munachulukitsa mawu anu ondinyoza+ ndipo ineyo ndinamva mawuwo.’+
42 “‘Mowabu adzawonongedwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu+ chifukwa wadzikweza pamaso pa Yehova.+
13 Anthu inu munalankhula modzitama kwa ine ndi pakamwa panu.+ Munachulukitsa mawu anu ondinyoza+ ndipo ineyo ndinamva mawuwo.’+