Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 19:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+

      Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+

      Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+

  • Yeremiya 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zimenezi zidzawachitikira chifukwa chakuti akhala akuchita zinthu zopanda nzeru mu Isiraeli,+ ndipo akupitiriza kuchita chigololo ndi akazi a anzawo.+ Komanso akupitiriza kulankhula zonama m’dzina langa. Iwo akulankhula mawu amene sindinawalamule kuti akanene.+

      “‘“Ine ndikuzidziwa zimenezi ndipo ndine mboni yake,”+ watero Yehova.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena