Yeremiya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+ Hoseya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+
9 Kodi mungamabe,+ kupha,+ kuchita chigololo,+ kulumbira monama,+ kufukiza nsembe zautsi kwa Baala+ ndi kutsatira milungu ina imene simunali kuidziwa,+
2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+