14 Mwa aneneri a ku Yerusalemu ndaona zinthu zoopsa.+ Iwo achita chigololo+ ndi kuchita zinthu mwachinyengo.+ Alimbikitsa anthu ochita zoipa kuti aliyense asafooke ndi kusiya+ kuchita zoipa zake. Kwa ine, onsewo akhala ngati Sodomu+ ndipo anthu okhala mumzindawu akhala ngati Gomora.”+