Ezekieli 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe unalankhula modzitama kwa ine ndipo unachulukitsa mawu ako ondinyoza.+ Ine ndinamva zonsezo.’