Ezekieli 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu inu munalankhula modzitama kwa ine ndi pakamwa panu.+ Munachulukitsa mawu anu ondinyoza+ ndipo ineyo ndinamva mawuwo.’+
13 Anthu inu munalankhula modzitama kwa ine ndi pakamwa panu.+ Munachulukitsa mawu anu ondinyoza+ ndipo ineyo ndinamva mawuwo.’+