Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,

      Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+

      Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+

      Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+

  • 2 Mbiri 32:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano musalole kuti Hezekiya akupusitseni+ kapena kukunyengererani+ chonchi ndipo musamukhulupirire, chifukwa palibe ufumu uliwonse kapena mulungu wa mtundu uliwonse wa anthu amene anatha kupulumutsa anthu akewo m’manja mwanga ndiponso m’manja mwa makolo anga. Ndiye mukuganiza kuti Mulungu wanu angakupulumutseni m’manja mwanga?’”+

  • Danieli 11:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 “Mfumuyo idzachita zofuna zake ndipo idzadzikweza ndi kudzikuza kuposa mulungu aliyense.+ Iyo idzalankhula zinthu zodabwitsa zotsutsana ndi Mulungu wa milungu.+ Idzapambana kufikira chidzudzulo champhamvu chitaperekedwa chonse,+ chifukwa chinthu chimene chakonzedwa chiyenera kuchitika.

  • Chivumbulutso 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chilombocho chinatsegula pakamwa pake n’kumanyoza Mulungu,+ dzina lake ndi malo ake okhala, ndiponso amene akukhala kumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena