Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Salimo 82:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Mulungu waima pakati pa msonkhano wake,+Ndipo akuweruza pakati pa milungu kuti:+ Salimo 136:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Mulungu wa milungu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+