Ekisodo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano ndadziwa kuti Yehova ndiye wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Zimenezi zinaoneka Aiguputo atasonyeza kudzikuza pamaso pa Aisiraeli.” 2 Mbiri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+ Danieli 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+
11 Tsopano ndadziwa kuti Yehova ndiye wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Zimenezi zinaoneka Aiguputo atasonyeza kudzikuza pamaso pa Aisiraeli.”
5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+
9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+