Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi,+ palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe.+

  • Danieli 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano Mulungu anawachititsa ana anayi amenewa kudziwa ndi kuzindikira zinthu zonse zolembedwa ndiponso anawapatsa nzeru.+ Danieli anali womvetsa bwino masomphenya ndi maloto amtundu uliwonse.+

  • Danieli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Koma kuli Mulungu kumwamba amene ndi Woulula zinsinsi,+ ndipo wakudziwitsani, inu Mfumu Nebukadinezara, zimene zidzachitike m’masiku otsiriza.+ Maloto anu ndi masomphenya amene munaona muli pabedi lanu ndi awa:

  • Danieli 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “‘Iwe Belitesazara mkulu wa ansembe ochita zamatsenga,+ ndikudziwa bwino kuti mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe+ ndipo palibe chinsinsi chimene umavutika nacho.+ Chotero ndiuze zimene ndinaona m’maloto anga ndi kumasulira kwake.+

  • Amosi 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena