Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+ 1 Akorinto 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano tikulankhula za nzeru kwa anthu okhwima mwauzimu,+ koma osati nzeru+ ya nthawi ino kapena ya olamulira a nthawi* ino+ amene adzawonongedwa.+
6 Tsopano tikulankhula za nzeru kwa anthu okhwima mwauzimu,+ koma osati nzeru+ ya nthawi ino kapena ya olamulira a nthawi* ino+ amene adzawonongedwa.+