Mateyu 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Yesu anawaitana n’kuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti olamulira a anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+
25 Koma Yesu anawaitana n’kuwauza kuti: “Inu mukudziwa kuti olamulira a anthu a mitundu ina amapondereza anthu awo ndipo akuluakulu amasonyeza mphamvu zawo pa iwo.+