1 Akorinto 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano tikulankhula za nzeru kwa anthu okhwima mwauzimu,+ koma osati nzeru+ ya nthawi ino kapena ya olamulira a nthawi* ino+ amene adzawonongedwa.+ 2 Akorinto 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sikuti ndife olamulira+ chikhulupiriro chanu, koma ndife antchito anzanu+ kuti mukhale ndi chimwemwe, pakuti ndinu okhazikika+ chifukwa cha chikhulupiriro chanu.+
6 Tsopano tikulankhula za nzeru kwa anthu okhwima mwauzimu,+ koma osati nzeru+ ya nthawi ino kapena ya olamulira a nthawi* ino+ amene adzawonongedwa.+
24 Sikuti ndife olamulira+ chikhulupiriro chanu, koma ndife antchito anzanu+ kuti mukhale ndi chimwemwe, pakuti ndinu okhazikika+ chifukwa cha chikhulupiriro chanu.+