Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Pamenepo Farao anafunsa antchito ake kuti: “Kodi pangapezekenso munthu wina wonga uyu, wokhala ndi mzimu wa Mulungu?”+

  • Danieli 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’kupita kwa nthawi, Danieli anaonetsa kuti anali wodziwa kugwira ntchito bwino+ kuposa nduna zonse zapamwamba ndi masatarapi onse, chifukwa anali ndi luso lodabwitsa+ ndipo mfumu inali kuganiza zomukweza kuti akhale pamwamba pa wina aliyense mu ufumuwo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena