Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Salimo 136:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yamikani Mbuye wa ambuye:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+