Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 86:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+ Salimo 95:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 135:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndikudziwa bwino kuti Yehova ndi wamkulu,+Ndipo Ambuye wathu ndi woposa milungu ina yonse.+
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
8 Inu Yehova, palibe mulungu wina amene angafanane ndi inu.+Ndipo palibe ntchito zilizonse zofanana ndi ntchito zanu.+
3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 135:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndikudziwa bwino kuti Yehova ndi wamkulu,+Ndipo Ambuye wathu ndi woposa milungu ina yonse.+