Salimo 48:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+ Salimo 95:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
48 Yehova ndi wamkulu ndi woyenera kutamandidwa kwambiri,+Mumzinda wa Mulungu wathu,+ m’phiri lake loyera.+
3 Pakuti Yehova ndi Mulungu wamkulu,+Ndiponso ndi Mfumu yaikulu kuposa milungu ina yonse.+ Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+