Yobu 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+Ndani angachite naye makani,* koma osavulala?+ Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Yeremiya 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+