Salimo 83:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+ Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+ Yeremiya 30:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pakuti ine ndili ndi iwe kuti ndikupulumutse,”+ watero Yehova. “Ndidzawononga anthu a mitundu yonse ya kumene ndinakubalalitsirani,+ koma iwe sindidzakuwononga.+ Ndidzakuwongolera pa mlingo woyenera chifukwa sindidzakusiya osakulanga.”+
4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+
8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+
11 “Pakuti ine ndili ndi iwe kuti ndikupulumutse,”+ watero Yehova. “Ndidzawononga anthu a mitundu yonse ya kumene ndinakubalalitsirani,+ koma iwe sindidzakuwononga.+ Ndidzakuwongolera pa mlingo woyenera chifukwa sindidzakusiya osakulanga.”+