Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+