Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 107:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Amadzandira ndipo amayenda peyupeyu ngati munthu woledzera,+

      Ndipo ngakhale nzeru zawo zonse zimasokonezeka.+

  • Miyambo 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Vinyo ndi wonyoza.+ Chakumwa choledzeretsa chimasokosera+ ndipo aliyense wosochera nacho alibe nzeru.+

  • Yesaya 28:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amenewanso asochera chifukwa cha vinyo. Akuyenda uku ndi uku chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Ansembe ndi aneneri+ asochera chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Asokonezeka chifukwa cha vinyo. Akuyenda uku ndi uku+ chifukwa cha chakumwa choledzeretsa. Sakuonanso bwino ndipo zochita zawo zikusonyeza kuti sakuganiza bwino.

  • Yeremiya 48:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 ‘Muledzeretseni+ anthu inu chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu wadzigwetsa ndipo wagubuduka m’masanzi ake,+ ndipo wakhaladi chinthu chotonzedwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena