Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pambuyo pake, iye anamwa vinyo ndi kuledzera naye.+ Kenako, ali m’hema wake, anavula zovala zake.

  • Salimo 107:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Amadzandira ndipo amayenda peyupeyu ngati munthu woledzera,+

      Ndipo ngakhale nzeru zawo zonse zimasokonezeka.+

  • Miyambo 23:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Usayang’ane vinyo akamaoneka wofiira, akamanyezimira m’kapu, akamatsetserekera kukhosi mwamyaa!

  • Yesaya 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena