-
Genesis 19:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Chotero, usiku uwunso anakhala akuwapatsa vinyo bambo awo kuti azimwa. Kenako, mwana wamng’ono uja anapita n’kukagona nawo. Koma kuyambira pamene mwanayo anabwera kudzagona nawo mpaka pamene anachoka, bambowo sanadziwe chilichonse.
-