Miyambo 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Monga galu amene wabwerera ku masanzi ake, wopusa amabwereza uchitsiru wake.+ 1 Akorinto 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+
32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+