Ekisodo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+ Mateyu 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+ 2 Petulo 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu+ wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso m’matope.”+
15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+
45 Ukatero umapita kukatenga mizimu ina 7 yoipa kwambiri kuposa umenewo.+ Ikalowa mkatimo imakhala mmenemo ndipo potsirizira pake zochita za munthuyo zimakhala zoipa kwambiri kuposa poyamba.+ Ndi mmenenso zidzakhalira ndi m’badwo woipawu.”+
22 Mwambi woona uja wakwaniritsidwa pa iwo. Mwambiwo umati: “Galu+ wabwerera kumasanzi ake, ndipo nkhumba imene inasambitsidwa yapita kukagubudukanso m’matope.”+