Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo mʼdzikolo.+Atsogoleri awo asocheretsa Iguputo pa chilichonse chimene akuchita,Ngati munthu woledzera amene akuterereka mʼmasanzi ake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Yesaya 1, ptsa. 202-203
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo mʼdzikolo.+Atsogoleri awo asocheretsa Iguputo pa chilichonse chimene akuchita,Ngati munthu woledzera amene akuterereka mʼmasanzi ake.