Yesaya 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Yesaya 1, ptsa. 202-203
14 Yehova waika mzimu wachisokonezo pakati pa dzikolo.+ Atsogoleri awo achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku m’zochita zake zonse, ngati munthu woledzera amene akuterereka m’masanzi ake.+