-
Yobu 12:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Alangizi okhulupirika amawasowetsa chonena,
Ndipo amachotsa kuzindikira kwa amuna achikulire,*
-
Yesaya 19:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Iwo adzafunsira kwa milungu yopanda pake,
Kwa anthu amatsenga, kwa olankhula ndi mizimu ndiponso kwa olosera zamʼtsogolo.+
-
-
-