Yesaya 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”? Yesaya 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.Akalonga a ku Nofi*+ apusitsidwa.Atsogoleri a mafuko ake asocheretsa Iguputo.
11 Akalonga a ku Zowani+ ndi opusa. Alangizi anzeru kwambiri a Farao, amapereka malangizo osathandiza.+ Koma zoona mungamuuze Farao kuti: “Ine ndine mbadwa ya anthu anzeru,Ndine mbadwa ya mafumu akale”?
13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.Akalonga a ku Nofi*+ apusitsidwa.Atsogoleri a mafuko ake asocheretsa Iguputo.