Yesaya 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:13 Yesaya 1, ptsa. 202-203
13 Akalonga a ku Zowani achita zopusa.+ Akalonga a ku Nofi+ anyengezedwa. Atsogoleri+ a mafuko achititsa Iguputo kuyenda uku ndi uku.