Salimo 78:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu anachita zodabwitsa pamaso pa makolo awo,+Mʼdziko la Iguputo, mʼdera la Zowani.+ Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani ndidzauwotcha ndi moto ndipo ndidzaweruza mzinda wa No.*+