Yeremiya 48:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Kodi Isiraeli sanasanduke chinthu chotonzedwa kwa inu?+ Kapena kodi anapezeka pakati pa mbala zenizeni?+ Inu munali kupukusa mitu moipidwa pamene munali kumunenera zinthu zoipa. Ezekieli 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+
27 “‘Kodi Isiraeli sanasanduke chinthu chotonzedwa kwa inu?+ Kapena kodi anapezeka pakati pa mbala zenizeni?+ Inu munali kupukusa mitu moipidwa pamene munali kumunenera zinthu zoipa.
8 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Popeza kuti Mowabu+ ndi Seiri+ anena kuti: “Taonani! Nyumba ya Yuda ili ngati mitundu ina yonse ya anthu,”+