Yesaya 65:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+ Machitidwe 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+
23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+
39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+