Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 59:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova wanena kuti: “Koma pangano langa ndi iwowo+ ndi ili:

      “Mzimu wanga umene uli pa iwe+ ndi mawu anga amene ndaika m’kamwa mwako,+ sizidzachoka m’kamwa mwako ndiponso m’kamwa mwa ana ako kapenanso m’kamwa mwa ana a ana ako, kuyambira panopa mpaka kalekale,” watero Yehova.+

  • Yesaya 66:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Pakuti monga momwe kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzakhalirebe pamaso panga,+ momwemonso ana anu+ ndi dzina lanu zidzakhalapo mpaka kalekale,”+ akutero Yehova.

  • Yeremiya 32:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndi kuwachititsa kuyenda m’njira imodzi kuti azindiopa nthawi zonse. Ndidzatero kuti iwo pamodzi ndi ana awo zinthu ziwayendere bwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena