Yesaya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+ Yohane 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+
2 Mzimu wa Yehova udzakhazikika pa iye,+ mzimu wanzeru,+ womvetsa zinthu,+ wolangiza, wamphamvu,+ wodziwa zinthu+ ndi woopa Yehova.+
33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+