Zekariya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mabwalo a mzindawo mudzadzaza anyamata ndi atsikana ndipo azidzasewera mmenemo.’”+ Luka 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Iwo ali ngati ana aang’ono amene akhala pansi mumsika n’kumafuulirana kuti, ‘Tinakuimbirani chitoliro, koma simunavine. Tinalira mofuula, koma inu simunalire.’+
32 Iwo ali ngati ana aang’ono amene akhala pansi mumsika n’kumafuulirana kuti, ‘Tinakuimbirani chitoliro, koma simunavine. Tinalira mofuula, koma inu simunalire.’+