Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 60:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+

  • Mika 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu amene anali kuyenda motsimphina ndidzawasonkhanitsanso pamodzi monga anthu otsala.+ Anthu amene anawachotsa m’dziko lawo ndi kuwapititsa kutali ndidzawasandutsa mtundu wamphamvu.+ Yehova adzawalamulira monga mfumu m’phiri la Ziyoni kuyambira nthawi imeneyo mpaka kalekale.+

  • Zefaniya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pa nthawi imeneyo ndidzaukira onse amene akukuzunza+ ndipo ndidzapulumutsa otsimphina.+ Anthu obalalitsidwa ndidzawasonkhanitsa pamodzi+ ndipo ndidzawachititsa kukhala otamandidwa komanso otchuka m’dziko lonse limene anachititsidwa manyazi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena