Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho Yehova Mulungu wanu adzakulowetsanidi m’dziko limene makolo anu analitenga kukhala lawo, ndipo inu mudzalitenga kukhala lanu. Pamenepo, adzakuchitirani zabwino ndi kukuchulukitsani kuposa makolo anu.+

  • Yesaya 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’masiku amene akubwerawo, Yakobo adzamera mizu n’kukhala wamphamvu ngati mtengo. Isiraeli+ adzakhala ngati mtengo waukulu wa maluwa ambiri. Iwo adzabereka zipatso panthaka ya dziko lonse lapansi.+

  • Yeremiya 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ine ndidzachulukitsa mbewu ya Davide mtumiki wanga ndi Alevi amene akunditumikira.+ Ndidzawachulukitsa mofanana ndi makamu akumwamba amene sangathe kuwerengedwa ndiponso mofanana ndi mchenga umene munthu sangathe kuuyeza.’”+

  • Zekariya 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Ndidzawaitana ndi likhweru+ ndi kuwasonkhanitsa pamodzi. Ndithu ine ndidzawawombola,+ ndipo iwo adzachuluka ngati anthu amene kale anali ambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena