Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 92:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anthu obzalidwa m’nyumba ya Yehova,+

      M’mabwalo a Mulungu wathu,+ adzakula mosangalala.

  • Yesaya 37:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Anthu a m’nyumba ya Yuda amene adzapulumuke, amene adzatsale,+ ndithu adzazika mizu pansi n’kubereka zipatso m’mwamba.+

  • Yesaya 60:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Wamng’ono adzasanduka anthu 1,000, ndipo wochepa adzasanduka mtundu wamphamvu.+ Ineyo Yehova ndidzafulumizitsa zimenezi pa nthawi yake.”+

  • Yeremiya 30:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kwa iwo kudzamveka mawu oyamikira ndi phokoso la kuseka kwa anthu.+ Ndidzawachulukitsa moti sadzakhala ochepa.+ Ndidzachulukitsa chiwerengero chawo moti sadzakhala kagulu kakang’ono ka anthu.+

  • Hoseya 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena