Deuteronomo 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+ 1 Mafumu 8:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Atero n’cholinga choti anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi adziwe+ kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso wina.+ Yesaya 45:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,
35 Inuyo mwasonyezedwa zinthu zimenezi kuti mudziwe kuti Yehova ndiye Mulungu woona,+ ndipo palibenso wina.+
60 Atero n’cholinga choti anthu a mitundu yonse ya padziko lapansi adziwe+ kuti Yehova ndi Mulungu woona.+ Palibenso wina.+
5 Ine ndine Yehova, ndipo palibenso wina.+ Palibenso Mulungu kupatulapo ine.+ Ndidzakumanga mwamphamvu m’chiuno mwako, ngakhale kuti sukundidziwa,