Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Yehova anachita zimenezi kuti mitundu yonse ya anthu a padziko lapansi idziwe kuti dzanja lake+ ndi lamphamvu,+ ndiponso kuti inu muzimuopadi Yehova Mulungu wanu nthawi zonse.’”+

  • 1 Samueli 17:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Lero Yehova akupereka m’manja mwanga,+ ndipo ndikupha ndi kukudula mutu. Lero ndipereka mitembo ya anthu a m’misasa ya Afilisiti kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.+ Anthu onse a padziko lapansi adzadziwa kuti Isiraeli ali ndi Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena