Yesaya 56:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu nyama zonse zakutchire, inu nyama zonse za m’nkhalango, bwerani mudzadye.+ Chivumbulutso 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,
17 Ndinaonanso mngelo ataimirira padzuwa. Iye anafuula ndi mawu okweza kwa mbalame+ zonse zouluka chapafupi m’mlengalenga, kuti: “Bwerani kuno, dzasonkhaneni ku phwando lalikulu la Mulungu la chakudya chamadzulo,