1 Yohane 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lamulo lakale+ limene mwakhala nalo kuyambira pa chiyambi.+ Lamulo lakale limeneli ndiwo mawu amene munamva. 1 Yohane 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+ 1 Yohane 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti uwu ndi uthenga umene munamva kuyambira pa chiyambi,+ kuti tizikondana,+
7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lamulo lakale+ limene mwakhala nalo kuyambira pa chiyambi.+ Lamulo lakale limeneli ndiwo mawu amene munamva.
24 Koma zimene inu munamva pa chiyambi zikhalebe mumtima mwanu.+ Zimene munamva pa chiyambi zikakhalabe mumtima mwanu, mudzakhalanso ogwirizana+ ndi Mwana ndi Atate.+