1 Yohane 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+ 2 Yohane 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tonse tizikondana.+ Sindikukulemberani zimenezi ngati munthu amene ndikukupatsani lamulo latsopano,+ koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.+
1 Tikukulemberani za iye amene analiko kuyambira pa chiyambi,+ amene amabweretsa mawu opatsa moyo,+ amene tamumva+ ndiponso kumuona ndi maso athu,+ amene tamuyang’anitsitsa+ mwachidwi ndi kumukhudza ndi manja athu.+
5Â Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tonse tizikondana.+ Sindikukulemberani zimenezi ngati munthu amene ndikukupatsani lamulo latsopano,+ koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.+