1 Yohane 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lamulo lakale+ limene mwakhala nalo kuyambira pa chiyambi.+ Lamulo lakale limeneli ndiwo mawu amene munamva.
7 Okondedwa, sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lamulo lakale+ limene mwakhala nalo kuyambira pa chiyambi.+ Lamulo lakale limeneli ndiwo mawu amene munamva.