Deuteronomo 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ana anu muwaphunzitsenso mawu amenewa, ndipo muzilankhula nawo za mawuwa mukakhala pansi m’nyumba mwanu, poyenda pamsewu, pogona ndi podzuka.+ Salimo 71:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+ Miyambo 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Lilime la wolungama ndilo siliva wabwino kwambiri.+ Mtima wa woipa ndi wopanda phindu.+
19 Ana anu muwaphunzitsenso mawu amenewa, ndipo muzilankhula nawo za mawuwa mukakhala pansi m’nyumba mwanu, poyenda pamsewu, pogona ndi podzuka.+
8 M’kamwa mwanga mwadzaza mawu otamanda inu,+Ndipo pakamwa panga pakunena za ulemerero wanu tsiku lonse.+