Salimo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ameneyo adzalandira madalitso kuchokera kwa Yehova,+Adzalandira chilungamo kuchokera kwa Mulungu wa chipulumutso chake.+ Salimo 88:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+
5 Ameneyo adzalandira madalitso kuchokera kwa Yehova,+Adzalandira chilungamo kuchokera kwa Mulungu wa chipulumutso chake.+
88 Inu Yehova, Mulungu wa chipulumutso changa,+Masana ndimafuula kwa inu,+Usikunso ndimafuula pamaso panu.+