1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+ Salimo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzafuulira Yehova mokweza,Ndipo iye adzandiyankha m’phiri lake loyera.+ [Seʹlah.] Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene analikonda.+
16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+